1 Mafumu 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Kuyambira tsiku limene ndinatulutsa anthu anga Aisiraeli mʼdziko la Iguputo, sindinasankhe mzinda mʼmafuko onse a Isiraeli womangako nyumba ya dzina langa kuti likhale kumeneko.+ Koma ndasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’
16 ‘Kuyambira tsiku limene ndinatulutsa anthu anga Aisiraeli mʼdziko la Iguputo, sindinasankhe mzinda mʼmafuko onse a Isiraeli womangako nyumba ya dzina langa kuti likhale kumeneko.+ Koma ndasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’