1 Mafumu 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye atakalamba,+ akazi akewa anapotoza mtima wake moti Solomo ankatsatira milungu ina+ ndipo sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu ngati mmene anachitira bambo ake Davide. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:4 Nsanja ya Olonda,7/1/2005, tsa. 29
4 Iye atakalamba,+ akazi akewa anapotoza mtima wake moti Solomo ankatsatira milungu ina+ ndipo sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu ngati mmene anachitira bambo ake Davide.