1 Mafumu 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yerobowamu anamanga nyumba zolambiriramo mʼmalo okwezeka. Ndipo anasankha anthu wamba, anthu amene sanali ana a Levi, kuti akhale ansembe.+
31 Yerobowamu anamanga nyumba zolambiriramo mʼmalo okwezeka. Ndipo anasankha anthu wamba, anthu amene sanali ana a Levi, kuti akhale ansembe.+