1 Mafumu 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako ndinangʼamba ufumu kuuchotsa kunyumba ya Davide nʼkukupatsa.+ Koma iwe sunakhale ngati Davide mtumiki wanga amene anasunga malamulo anga, kunditsatira ndi mtima wake wonse ndiponso kuchita zinthu zoyenera zokhazokha pamaso panga.+
8 Kenako ndinangʼamba ufumu kuuchotsa kunyumba ya Davide nʼkukupatsa.+ Koma iwe sunakhale ngati Davide mtumiki wanga amene anasunga malamulo anga, kunditsatira ndi mtima wake wonse ndiponso kuchita zinthu zoyenera zokhazokha pamaso panga.+