1 Mafumu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anayenda masiku 40, masana ndi usiku, mpaka anakafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:8 Tsanzirani, ptsa. 103-104 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, ptsa. 20-21
8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anayenda masiku 40, masana ndi usiku, mpaka anakafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+