2 Mafumu 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti Aisiraeliwo sanamvere mawu a Yehova Mulungu wawo, koma anaphwanya pangano lake ndi zonse zimene Mose mtumiki wa Yehova anawalamula.+ Iwo sanamvere kapena kutsatira zimenezi.
12 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti Aisiraeliwo sanamvere mawu a Yehova Mulungu wawo, koma anaphwanya pangano lake ndi zonse zimene Mose mtumiki wa Yehova anawalamula.+ Iwo sanamvere kapena kutsatira zimenezi.