2 Mafumu 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 komanso chifukwa cha anthu ambiri osalakwa amene anawapha,+ moti anadzaza Yerusalemu ndi magazi a anthu osalakwa ndipo Yehova sanafune kukhululuka.+
4 komanso chifukwa cha anthu ambiri osalakwa amene anawapha,+ moti anadzaza Yerusalemu ndi magazi a anthu osalakwa ndipo Yehova sanafune kukhululuka.+