2 Mafumu 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼmwezi wa 5, pa tsiku la 7 la mweziwo, chomwe chinali chaka cha 19 cha Mfumu Nebukadinezara ya ku Babulo, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu, mtumiki wa mfumu ya Babulo, anabwera ku Yerusalemu.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:8 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 11
8 Mʼmwezi wa 5, pa tsiku la 7 la mweziwo, chomwe chinali chaka cha 19 cha Mfumu Nebukadinezara ya ku Babulo, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu, mtumiki wa mfumu ya Babulo, anabwera ku Yerusalemu.+