2 Mafumu 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tikati, ‘Tiyeni tilowe mumzinda,’ tikafa ndi njala.+ Tikatinso tikhale pano, tifa. Ndiye tiyeni tikalowe mumsasa wa Asiriya. Akakapanda kutipha, tikakhala ndi moyo koma akakatipha, basi tikafa.”
4 Tikati, ‘Tiyeni tilowe mumzinda,’ tikafa ndi njala.+ Tikatinso tikhale pano, tifa. Ndiye tiyeni tikalowe mumsasa wa Asiriya. Akakapanda kutipha, tikakhala ndi moyo koma akakatipha, basi tikafa.”