2 Mafumu 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Atatero, analowa mʼnyumba ndipo anayamba kudya ndi kumwa, kenako anati: “Mutengeni mayi wotembereredwayu mukamuike mʼmanda, paja ndi mwana wa mfumu.”+
34 Atatero, analowa mʼnyumba ndipo anayamba kudya ndi kumwa, kenako anati: “Mutengeni mayi wotembereredwayu mukamuike mʼmanda, paja ndi mwana wa mfumu.”+