2 Mafumu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komabe iye sanasiye kuchita machimo amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati. Machimo ake anali akuti sanachotse mwana wa ngʼombe wagolide amene anali ku Beteli komanso amene anali ku Dani.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:29 Nsanja ya Olonda,11/15/2011, tsa. 5
29 Komabe iye sanasiye kuchita machimo amene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati. Machimo ake anali akuti sanachotse mwana wa ngʼombe wagolide amene anali ku Beteli komanso amene anali ku Dani.+