2 Mafumu 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehoasi+ anakhala mfumu mʼchaka cha 7 cha Yehu+ ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 40. Mayi ake anali a ku Beere-seba+ ndipo dzina lawo linali Zibiya.
12 Yehoasi+ anakhala mfumu mʼchaka cha 7 cha Yehu+ ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 40. Mayi ake anali a ku Beere-seba+ ndipo dzina lawo linali Zibiya.