2 Mafumu 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anayenda mʼnjira ya mafumu a Isiraeli+ ndipo anafika mpaka potentha* pamoto mwana wake wamwamuna,+ potsatira zinthu zonyansa zimene anthu a mitundu ina ankachita+ amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:3 Yesaya 1, ptsa. 8-9 Nsanja ya Olonda,7/15/1997, tsa. 14
3 Anayenda mʼnjira ya mafumu a Isiraeli+ ndipo anafika mpaka potentha* pamoto mwana wake wamwamuna,+ potsatira zinthu zonyansa zimene anthu a mitundu ina ankachita+ amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli.