1 Mbiri 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno tikatenge Likasa+ la Mulungu wathu nʼkubwera nalo kuno.” Ananena zimenezi chifukwa mʼmasiku a Sauli likasalo silinkasamalidwa.+
3 Ndiyeno tikatenge Likasa+ la Mulungu wathu nʼkubwera nalo kuno.” Ananena zimenezi chifukwa mʼmasiku a Sauli likasalo silinkasamalidwa.+