1 Mbiri 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho, Solomo anakhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu mʼmalo mwa Davide bambo ake ndipo zinthu zinkamuyendera bwino. Aisiraeli onse ankamumvera. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:23 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32
23 Choncho, Solomo anakhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu mʼmalo mwa Davide bambo ake ndipo zinthu zinkamuyendera bwino. Aisiraeli onse ankamumvera.