-
2 Mbiri 11:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mʼmizinda yonse anaikamo zishango zazikulu ndi mikondo ingʼonoingʼono. Mizindayo anailimbitsa kwambiri ndipo iye anapitiriza kulamulira Yuda ndi Benjamini.
-