2 Mbiri 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Rehobowamu anakwatira Mahalati mwana wamkazi wa Yerimoti mwana wa Davide. Amayi ake a Mahalati anali Abihaili mwana wamkazi wa Eliyabu mwana wa Jese.+
18 Rehobowamu anakwatira Mahalati mwana wamkazi wa Yerimoti mwana wa Davide. Amayi ake a Mahalati anali Abihaili mwana wamkazi wa Eliyabu mwana wa Jese.+