2 Mbiri 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imeneyo, wamasomphenya Haneni+ anapita kwa Asa mfumu ya Yuda nʼkumuuza kuti: “Chifukwa chakuti munadalira mfumu ya Siriya, osadalira Yehova Mulungu wanu, simunagonjetse asilikali a mfumu ya Siriya.+
7 Pa nthawi imeneyo, wamasomphenya Haneni+ anapita kwa Asa mfumu ya Yuda nʼkumuuza kuti: “Chifukwa chakuti munadalira mfumu ya Siriya, osadalira Yehova Mulungu wanu, simunagonjetse asilikali a mfumu ya Siriya.+