2 Mbiri 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Asilikaliwo atachoka (nʼkumusiya atavulala kwambiri), atumiki ake anamʼkonzera chiwembu chifukwa anapha ana* a wansembe Yehoyada.+ Iwo anamuphera pabedi lake.+ Kenako anamuika mʼmanda mu Mzinda wa Davide+ koma sanamuike mʼmanda a mafumu.+
25 Asilikaliwo atachoka (nʼkumusiya atavulala kwambiri), atumiki ake anamʼkonzera chiwembu chifukwa anapha ana* a wansembe Yehoyada.+ Iwo anamuphera pabedi lake.+ Kenako anamuika mʼmanda mu Mzinda wa Davide+ koma sanamuike mʼmanda a mafumu.+