5 Ndiyeno anayamba kupereka nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku,+ nsembe ya masiku amene mwezi watsopano waoneka+ ndi nsembe za pa zikondwerero zopatulika+ za Yehova. Anaperekanso nsembe za aliyense amene anapereka chopereka chaufulu+ kwa Yehova ndi mtima wonse.