Ezara 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndaikanso lamulo lakuti aliyense wophwanya lamulo limeneli, thabwa* lidzachotsedwe panyumba yake ndipo iye adzapachikidwe pathabwalo. Komanso nyumba yake idzasandutsidwa chimbudzi* cha aliyense chifukwa cha zimenezi.
11 Ndaikanso lamulo lakuti aliyense wophwanya lamulo limeneli, thabwa* lidzachotsedwe panyumba yake ndipo iye adzapachikidwe pathabwalo. Komanso nyumba yake idzasandutsidwa chimbudzi* cha aliyense chifukwa cha zimenezi.