Ezara 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anapereka nsembe ngʼombe zamphongo 100, nkhosa zamphongo 200 ndi ana a nkhosa amphongo 400. Anaperekanso mbuzi zamphongo 12 za nsembe yamachimo ya Aisiraeli onse, mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a Isiraeli.+
17 Iwo anapereka nsembe ngʼombe zamphongo 100, nkhosa zamphongo 200 ndi ana a nkhosa amphongo 400. Anaperekanso mbuzi zamphongo 12 za nsembe yamachimo ya Aisiraeli onse, mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a Isiraeli.+