Ezara 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa chakuti ansembe ndi Alevi anadziyeretsa+ ndipo palibe anatsala, onse anali oyera. Choncho Aleviwo anapha nyama ya Pasika ya anthu onse amene anachokera ku ukapolo, ya abale awo ansembe ndiponso yawo.
20 Chifukwa chakuti ansembe ndi Alevi anadziyeretsa+ ndipo palibe anatsala, onse anali oyera. Choncho Aleviwo anapha nyama ya Pasika ya anthu onse amene anachokera ku ukapolo, ya abale awo ansembe ndiponso yawo.