22 Kwa masiku 7, iwo anachita Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa+ mosangalala chifukwa Yehova anawachititsa kuti asangalale. Iye anachititsa kuti mfumu ya Asuri iwakomere mtima+ nʼkuwathandiza pa ntchito yomanga nyumba ya Mulungu woona, Mulungu wa Isiraeli.