Salimo 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngakhale madzi amʼnyanjayo atawinduka nʼkuchita thovu,+Ndiponso ngakhale mapiri atagwedezeka chifukwa cha kuwinduka kwa nyanjayo. (Selah)
3 Ngakhale madzi amʼnyanjayo atawinduka nʼkuchita thovu,+Ndiponso ngakhale mapiri atagwedezeka chifukwa cha kuwinduka kwa nyanjayo. (Selah)