Salimo 66:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa inu Mulungu mwatifufuza.+Mwatiyenga ngati mmene amayengera siliva.