Salimo 68:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa cha kachisi wanu yemwe ali ku Yerusalemu,+Mafumu adzabweretsa mphatso kwa inu.+