Salimo 74:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumbukirani anthu* amene munawatenga kalekale kuti akhale anu,+Fuko limene munaliwombola kuti likhale cholowa chanu.+ Kumbukirani phiri la Ziyoni kumene inu mumakhala.+
2 Kumbukirani anthu* amene munawatenga kalekale kuti akhale anu,+Fuko limene munaliwombola kuti likhale cholowa chanu.+ Kumbukirani phiri la Ziyoni kumene inu mumakhala.+