Salimo 82:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyamukani inu Mulungu, ndipo muweruze dziko lapansi,+Chifukwa mitundu yonse ya anthu ndi yanu.