Salimo 83:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwachinsinsi komanso mochenjera iwo amakonzera chiwembu anthu anu.Iwo amakonzera chiwembu anthu anu omwe ndi amtengo wapatali.*
3 Mwachinsinsi komanso mochenjera iwo amakonzera chiwembu anthu anu.Iwo amakonzera chiwembu anthu anu omwe ndi amtengo wapatali.*