-
Salimo 84:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ngakhale mbalame zapeza malo okhala kumeneko
Ndipo namzeze wadzimangira chisa chake,
Mmene amasamaliramo ana ake
Pafupi ndi guwa lanu lansembe lalikulu, inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,
Mfumu yanga ndi Mulungu wanga!
-