Salimo 147:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Imbirani amene amaphimba mapiri ndi mitambo,Amene amapereka mvula padziko lapansi,+Amenenso amameretsa udzu+ mʼmapiri. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 147:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2017, tsa. 19
8 Imbirani amene amaphimba mapiri ndi mitambo,Amene amapereka mvula padziko lapansi,+Amenenso amameretsa udzu+ mʼmapiri.