Miyambo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwana wanga, tchera makutu ako ku mawu anga anzeru. Mvetsera mosamala zimene ndikukuphunzitsa zokhudza kukhala wozindikira,+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 28
5 Mwana wanga, tchera makutu ako ku mawu anga anzeru. Mvetsera mosamala zimene ndikukuphunzitsa zokhudza kukhala wozindikira,+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 28