Miyambo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndi bwino kusankha dzina labwino* kusiyana ndi chuma chochuluka.+Kulemekezedwa* nʼkwabwino kuposa siliva ndi golide. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:1 Galamukani!,Na. 4 2017, tsa. 9
22 Ndi bwino kusankha dzina labwino* kusiyana ndi chuma chochuluka.+Kulemekezedwa* nʼkwabwino kuposa siliva ndi golide.