Mlaliki 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ntchentche zakufa nʼzimene zimachititsa kuti mafuta a munthu wopanga mafuta onunkhira awole nʼkuyamba kununkha. Mofanana ndi zimenezi uchitsiru pangʼono umawononga mbiri ya munthu amene amaoneka kuti ndi wanzeru komanso wolemekezeka.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 16 Galamukani!,3/8/2001, ptsa. 19-20
10 Ntchentche zakufa nʼzimene zimachititsa kuti mafuta a munthu wopanga mafuta onunkhira awole nʼkuyamba kununkha. Mofanana ndi zimenezi uchitsiru pangʼono umawononga mbiri ya munthu amene amaoneka kuti ndi wanzeru komanso wolemekezeka.+