-
Yesaya 9:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba
Dzikolo lawotchedwa ndi moto,
Ndipo anthuwo adzakhala ngati nkhuni zokolezera motowo.
Palibe amene adzapulumutse ngakhale mʼbale wake.
-