Yesaya 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa mumzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri mudzakhala mopanda anthu.Malo odyetserako ziweto adzasiyidwa ndipo adzakhala opanda kanthu ngati chipululu.+ Kumeneko mwana wa ngʼombe azidzadya msipu ndiponso kugona pansiNdipo iye adzadya nthambi zake.+
10 Chifukwa mumzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri mudzakhala mopanda anthu.Malo odyetserako ziweto adzasiyidwa ndipo adzakhala opanda kanthu ngati chipululu.+ Kumeneko mwana wa ngʼombe azidzadya msipu ndiponso kugona pansiNdipo iye adzadya nthambi zake.+