Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:6 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 27 Yesaya 2, ptsa. 64-65
6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+