Yesaya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:22 Yesaya 2, ptsa. 69-70
22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+