Yesaya 54:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa cha mkwiyo wanga waukulu ndinakubisira nkhope yanga kwa kanthawi,+Koma chifukwa cha chikondi changa chokhulupirika chimene sichidzatha ndidzakuchitira chifundo,”+ akutero Yehova, Wokuwombola.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:8 Yesaya 2, ptsa. 224-226
8 Chifukwa cha mkwiyo wanga waukulu ndinakubisira nkhope yanga kwa kanthawi,+Koma chifukwa cha chikondi changa chokhulupirika chimene sichidzatha ndidzakuchitira chifundo,”+ akutero Yehova, Wokuwombola.+