3 Yeremiya analandiranso mawuwo mʼmasiku a Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda mpaka kumapeto kwa chaka cha 11 cha ulamuliro wa Zedekiya+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, komanso mpaka pamene anthu a mu Yerusalemu anatengedwa kupita ku ukapolo mʼmwezi wa 5.+