Yeremiya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimene Yehova wanena kwa anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu ndi izi: “Limani minda panthaka yabwino,Ndipo musapitirize kudzala mbewu pakati pa minga.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 9
3 Zimene Yehova wanena kwa anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu ndi izi: “Limani minda panthaka yabwino,Ndipo musapitirize kudzala mbewu pakati pa minga.+