Yeremiya 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wanena kuti: “Imani pamphambano kuti muone. Funsani zokhudza njira zakale,Funsani kuti mudziwe kumene kuli njira yabwino nʼkuyenda mmenemo,+Kuti mupeze mpumulo.” Koma iwo akunena kuti: “Ife sitiyenda mʼnjira imeneyo.”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:16 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 1011/1/2005, tsa. 23-25
16 Yehova wanena kuti: “Imani pamphambano kuti muone. Funsani zokhudza njira zakale,Funsani kuti mudziwe kumene kuli njira yabwino nʼkuyenda mmenemo,+Kuti mupeze mpumulo.” Koma iwo akunena kuti: “Ife sitiyenda mʼnjira imeneyo.”+