Yeremiya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi nyumba iyi, imene imatchedwa ndi dzina langa, mwayamba kuiona ngati phanga la achifwamba?+ Inetu ndaona zimene mukuchita,” akutero Yehova. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:11 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 12
11 Kodi nyumba iyi, imene imatchedwa ndi dzina langa, mwayamba kuiona ngati phanga la achifwamba?+ Inetu ndaona zimene mukuchita,” akutero Yehova.