Yeremiya 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu amʼdzikoli adzafa, kaya ndi olemekezeka kapena onyozeka. Sadzaikidwa mʼmanda,Palibe aliyense amene adzalire maliro awo,Kapena kudzichekacheka komanso kumeta mpala chifukwa cha iwo.*
6 ‘Anthu amʼdzikoli adzafa, kaya ndi olemekezeka kapena onyozeka. Sadzaikidwa mʼmanda,Palibe aliyense amene adzalire maliro awo,Kapena kudzichekacheka komanso kumeta mpala chifukwa cha iwo.*