Yeremiya 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mitundu yonse ya anthu idzatumikira iyeyo, mwana wake wamwamuna ndi mdzukulu wake mpaka idzafike nthawi yoti ufumu wake uthe.+ Pa nthawi imeneyo, mitundu yambiri ya anthu ndi mafumu amphamvu adzamupangitsa kuti akhale kapolo wawo.’+
7 Mitundu yonse ya anthu idzatumikira iyeyo, mwana wake wamwamuna ndi mdzukulu wake mpaka idzafike nthawi yoti ufumu wake uthe.+ Pa nthawi imeneyo, mitundu yambiri ya anthu ndi mafumu amphamvu adzamupangitsa kuti akhale kapolo wawo.’+