Yeremiya 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ‘Ine sindinawatume,’ akutero Yehova, ‘koma iwo akulosera zabodza mʼdzina langa. Mukawamvera ndidzakubalalitsani ndipo ndidzawononga inuyo limodzi ndi aneneri amene akulosera kwa inu.’”+
15 ‘Ine sindinawatume,’ akutero Yehova, ‘koma iwo akulosera zabodza mʼdzina langa. Mukawamvera ndidzakubalalitsani ndipo ndidzawononga inuyo limodzi ndi aneneri amene akulosera kwa inu.’”+