Yeremiya 50:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa mtundu wina wa anthu wabwera kudzamuukira kuchokera kumpoto.+ Mtundu umenewu wasandutsa dziko lake kukhala chinthu chochititsa mantha.Palibe aliyense amene akukhala mʼdzikoli. Anthu ndiponso ziweto zathawa.Zathawira kutali.”
3 Chifukwa mtundu wina wa anthu wabwera kudzamuukira kuchokera kumpoto.+ Mtundu umenewu wasandutsa dziko lake kukhala chinthu chochititsa mantha.Palibe aliyense amene akukhala mʼdzikoli. Anthu ndiponso ziweto zathawa.Zathawira kutali.”