22 Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni, chilango chimene anakupatsa chifukwa cha zolakwa zako chatha.
Sadzakutenganso kupita nawe ku ukapolo.+
Koma Mulungu adzatembenukira kwa iwe, mwana wamkazi wa Edomu, kuti aone zolakwa zako.
Machimo ako adzawaika poyera.+