Ezekieli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako mkwiyo wanga udzatha komanso ukali wanga pa iwo udzachepa ndipo ndidzakhutira.+ Ndikadzamaliza kuwasonyeza ukali wanga, iwo adzadziwa kuti ine Yehova ndalankhula chifukwa ndimafuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha basi.+
13 Kenako mkwiyo wanga udzatha komanso ukali wanga pa iwo udzachepa ndipo ndidzakhutira.+ Ndikadzamaliza kuwasonyeza ukali wanga, iwo adzadziwa kuti ine Yehova ndalankhula chifukwa ndimafuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha basi.+